Pamene Iye anali chilankhulire ndi makamu, onani, amake ndi abale ake anaima panja, nafuna kulankhula naye.
Machitidwe a Atumwi 22:2 - Buku Lopatulika Ndipo pakumva kuti analankhula nao m'chinenedwe cha Chihebri, anaposa kukhala chete; ndipo anati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pakumva kuti analankhula nao m'chinenedwe cha Chihebri, anaposa kukhala chete; ndipo anati: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene iwo adamumva akulankhula nawo pa Chiyuda, adakhala chete kopambana. Tsono Paulo anati, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atamva iye akuyankhula Chihebri, anakhala chete. Kenaka Paulo anati, |
Pamene Iye anali chilankhulire ndi makamu, onani, amake ndi abale ake anaima panja, nafuna kulankhula naye.
Ndipo m'mene adamlola, Paulo anaimirira pamakwerero, natambalitsira anthu dzanja; ndipo pokhala chete onse, analankhula nao m'chinenedwe cha Chihebri, nanena: