Machitidwe a Atumwi 2:16 - Buku Lopatulika komatu ichi ndi chimene chinanenedwa ndi mneneri Yowele, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 komatu ichi ndi chimene chinanenedwa ndi mneneri Yowele, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma zimenezi ndi zomwe mneneri Yowele adalosa kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma izi ndi zimene ananena Mneneri Yoweli kuti: |
Ndipo kudzali m'masiku otsiriza, anena Mulungu, ndidzathira cha Mzimu wanga pa thupi lililonse, ndipo ana anu aamuna, ndi aakazi adzanenera, ndipo anyamata anu adzaona masomphenya, ndi akulu anu adzalota maloto;