Koma Ayuda anadukidwa mtima, natenga anthu ena oipa achabe a pabwalo, nasonkhanitsa khamu la anthu, nachititsa phokoso m'mzinda; ndipo anagumukira kunyumba ya Yasoni, nafuna kuwatulutsira kwa anthu.
Machitidwe a Atumwi 17:9 - Buku Lopatulika Ndipo pamene analandira chikole kwa Yasoni ndi enawo, anawamasula. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pamene analandira chikole kwa Yasoni ndi enawo, anawamasula. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Yasoni ndi anzake aja atalipira mlanduwo, akuluwo adaŵamasula. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo analipiritsa Yasoni ndi anzakewo ndipo anawamasula. |
Koma Ayuda anadukidwa mtima, natenga anthu ena oipa achabe a pabwalo, nasonkhanitsa khamu la anthu, nachititsa phokoso m'mzinda; ndipo anagumukira kunyumba ya Yasoni, nafuna kuwatulutsira kwa anthu.