chimenecho ndidachipenyetsetsa ndinachilingirira, ndipo ndinaona nyama za miyendo inai za padziko ndi zilombo, ndi zokwawa, ndi mbalame za m'mlengalenga.
Machitidwe a Atumwi 11:7 - Buku Lopatulika Ndipo ndinamvanso mau akunena ndi ine, Tauka Petro; ipha, nudye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ndinamvanso mau akunena ndi ine, Tauka Petro; ipha, nudye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono ndidamva mau ondiwuza kuti, ‘Petro dzuka, ipha, udye.’ Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka ine ndinamva mawu akuti, ‘Petro, Imirira. Ipha, nudye.’ |
chimenecho ndidachipenyetsetsa ndinachilingirira, ndipo ndinaona nyama za miyendo inai za padziko ndi zilombo, ndi zokwawa, ndi mbalame za m'mlengalenga.
Koma ndinati, Iaitu, Ambuye; pakuti kanthu wamba, kapena konyansa sikanalowe m'kamwa mwanga ndi kale lonse.
Pakuti cholengedwa chonse cha Mulungu nchabwino, ndipo palibe kanthu kayenera kutayika, ngati kalandiridwa ndi chiyamiko;