Machitidwe a Atumwi 11:4 - Buku Lopatulika Koma Petro anayamba kuwafotokozera chilongosolere, nanena, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma Petro anayamba kuwafotokozera chilongosolere, nanena, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Apo Petro adayamba kuŵafotokozera mwatsatanetsatane zimene zidachitika. Adati, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma Petro anayamba kuwafotokozera zonse mwatsatanetsatane momwe zinachitikira kuti, |
ndipo sanalankhule nao wopanda fanizo: koma m'tseri anatanthauzira zonse kwa ophunzira ake.
kuyambira pachiyambi, ndinayesa nkokoma inenso, amene ndinalondalonda mosamalitsa zinthu zonse kuyambira pachiyambi, kulembera kwa iwe tsatanetsatane, Teofilo wabwinotu iwe;
Pamene anafika nasonkhanitsa Mpingo anabwerezanso zomwe Mulungu anachita nao, kuti anatsegulira amitundu pa khomo la chikhulupiriro.