Luka 9:17 - Buku Lopatulika Ndipo anadya, nakhuta onsewo; natola makombo, madengu khumi ndi awiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anadya, nakhuta onsewo; natola makombo, madengu khumi ndi awiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu onse aja adadya nakhuta. Ndipo ophunzira aja adatola zotsala, nkudzaza madengu khumi ndi aŵiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Onse anadya nakhuta, ndipo ophunzira ake anatolera madengu khumi ndi awiri odzaza ndi nyenyeswa zomwe zinatsala. |
Ndipo Iye, m'mene anatenga mikate isanu ija ndi nsomba ziwiri anayang'ana kumwamba, nazidalitsa, nanyema, napatsa ophunzira apereke kwa anthuwo.