Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Luka 8:36 - Buku Lopatulika

Ndipo amene anaona anawauza iwo machiritsidwe ake a wogwidwa chiwandayo.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Ndipo amene anaona anawauza iwo machiritsidwe ake a wogwidwa chiwandayo.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Anzao amene adaaonerera zonse zikuchitika, adaŵasimbira m'mene munthu wamizimuyo adaamchiritsira.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Amene anaona izi anawuza anthu mmene munthu wogwidwa ndi ziwandayo anachiritsidwira.

Onani mutuwo



Luka 8:36
2 Mawu Ofanana  

Ndipo mbiri yake inabuka ku Siriya konse: ndipo anatengera kwa Iye onse akudwala, ogwidwa ndi nthenda ndi mazunzo a mitundumitundu, ndi ogwidwa ndi ziwanda, ndi akhunyu, ndi amanjenje; ndipo Iye anawachiritsa.


Ndipo anthu aunyinji onse a dziko la Agerasa loyandikira anamfunsa Iye achoke kwa iwo; chifukwa anagwidwa ndi mantha aakulu. Ndipo Iye analowa m'ngalawa, nabwerera.