Luka 7:18 - Buku Lopatulika Ndipo ophunzira a Yohane anamuuza iye zonsezi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ophunzira a Yohane anamuuza iye zonsezi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ophunzira a Yohane adamsimbira zonsezi Yohaneyo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo ophunzira a Yohane anamuwuza Yohaneyo zinthu zonsezi. Atayitana awiri a ophunzirawo, |
Ndipo anadza kwa Yohane, nati kwa iye, Rabi, Iye amene anali ndi inu tsidya lija la Yordani, amene munamchitira umboni, taonani yemweyu abatiza, ndipo anthu onse alinkudza kwa Iye.