Ndipo Yesu anayendayenda mu Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira Uthenga Wabwino wa Ufumu, nachiritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.
Luka 4:44 - Buku Lopatulika Ndipo Iye analikulalikira m'masunagoge a ku Yudeya. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Iye analikulalikira m'masunagoge a ku Yudeya. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero Iye ankalalika m'nyumba zamapemphero za ku Yudeya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Iye anapitirirabe kulalikira mʼmasunagoge a ku Yudeya. |
Ndipo Yesu anayendayenda mu Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira Uthenga Wabwino wa Ufumu, nachiritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.
Ndipo panali, pakumkanikiza khamu la anthu, kudzamva mau a Mulungu, Iye analikuimirira m'mbali mwa nyanja ya Genesarete;