Ndipo Iye anatsika nadza ku Kapernao, ndiwo mzinda wa ku Galileya. Ndipo analikuwaphunzitsa iwo pa Sabata; ndipo anadabwa ndi chiphunzitso chake;
Luka 4:30 - Buku Lopatulika Koma Iye anapyola pakati pao, nachokapo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma Iye anapyola pakati pao, nachokapo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa koma Iye adangodzadutsa pakati pao, nkumapita. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma Iye anangoyenda pakati pa gulu la anthulo nachokapo. |
Ndipo Iye anatsika nadza ku Kapernao, ndiwo mzinda wa ku Galileya. Ndipo analikuwaphunzitsa iwo pa Sabata; ndipo anadabwa ndi chiphunzitso chake;