Luka 4:10 - Buku Lopatulika pakuti kwalembedwa kuti, Adzalamula angelo ake za iwe, kuti akutchinjirize. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 pakuti kwalembedwa kuti, Adzalamula angelo ake za iwe, kuti akutchinjirize. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Paja Malembo akuti, “ ‘Mulungu adzalamula angelo ake kuti akusamaleni.’ Ndiponso, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pakuti kwalembedwa, “Adzalamulira angelo ake za iwe kuti akutchinjirize mosamala; |
Ndipo mdierekezi anati kwa Iye, Ngati muli Mwana wa Mulungu, uzani mwala uwu usanduke mkate.
Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iye, Kwalembedwa, kuti, Ambuye Mulungu wako uzimgwadira, ndipo Iye yekhayekha uzimtumikira.
Kodi siili yonse mizimu yotumikira, yotumidwa kuti itumikire iwo amene adzalowa chipulumutso?