nabwera kuchokera kumanda, nafotokozera zonse khumi ndi mmodziwo, ndi otsala onse omwe.
Luka 24:8 - Buku Lopatulika Ndipo anakumbukira mau ake, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anakumbukira mau ake, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Apo akazi aja adaŵakumbukiradi mauwo, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo anakumbukira mawu ake. |
nabwera kuchokera kumanda, nafotokozera zonse khumi ndi mmodziwo, ndi otsala onse omwe.
Izi sanazidziwe ophunzira ake poyamba; koma pamene Yesu analemekezedwa, pamenepo anakumbukira kuti izi zinalembedwa za Iye, ndi kuti adamchitira Iye izi.
Koma Nkhosweyo, Mzimu Woyera, amene Atate adzamtuma m'dzina langa, Iyeyo adzaphunzitsa inu zonse, nadzakumbutsa inu zinthu zonse zimene ndinanena kwa inu.