ndi kuwaphunzitsa, asunge zinthu zonse zimene ndinakulamulani inu; ndipo onani, Ine ndili pamodzi ndi inu masiku onse, kufikira chimaliziro cha nthawi ya pansi pano.
Luka 24:53 - Buku Lopatulika ndipo anakhala chikhalire mu Kachisi, nalikuyamika Mulungu. Amen. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo anakhala chikhalire m'Kachisi, nalikuyamika Mulungu. Amen. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono ankasonkhana m'Nyumba ya Mulungu nthaŵi ndi nthaŵi akutamanda Mulungu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo iwo anakhalabe ku Nyumba ya Mulungu, akulemekeza Mulungu. |
ndi kuwaphunzitsa, asunge zinthu zonse zimene ndinakulamulani inu; ndipo onani, Ine ndili pamodzi ndi inu masiku onse, kufikira chimaliziro cha nthawi ya pansi pano.
Ndipo iwowa anatuluka, nalalikira ponseponse, ndipo Ambuye anachita nao pamodzi, natsimikiza mau ndi zizindikiro zakutsatapo. Amen.