Luka 24:16 - Buku Lopatulika Koma maso ao anagwidwa kuti asamzindikire Iye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma maso ao anagwidwa kuti asamzindikire Iye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma maso ao adaachita chidima, mwakuti sadamzindikire. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero koma iwo sanamuzindikire. |
Ndipo zitatha izi, anaonekanso Iye m'maonekedwe ena kwa awiri a iwo alikuyenda kupita kumidzi.
Ndipo anati kwa iwo, Mau awa ndi otani mulandizanawo poyendayenda? Ndipo anaima ndi nkhope zao zachisoni.
Ndipo maso ao anatseguka, ndipo anamzindikira Iye; ndipo anawakanganukira Iye, nawachokera.
M'mene adanena izi, anacheuka m'mbuyo, naona Yesu ali chilili, ndipo sanadziwe kuti ndiye Yesu.
Koma pakuyamba kucha, Yesu anaimirira pambali pa nyanja, komatu ophunzirawo sanadziwe kuti ndiye Yesu.