Ndipo pamene kunacha, bungwe la akulu a anthu linasonkhana, ndiwo ansembe aakulu ndi alembi; ndipo anapita naye kubwalo lao,
Luka 23:1 - Buku Lopatulika Ndipo khamu lonselo linanyamuka kupita naye kwa Pilato. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo khamu lonselo linanyamuka kupita naye kwa Pilato. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Gulu lonse lija lidanyamuka nkupita naye Yesu kwa Pilato. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka gulu lonse la anthuwo linayimirira ndi kumutengera kwa Pilato. |
Ndipo pamene kunacha, bungwe la akulu a anthu linasonkhana, ndiwo ansembe aakulu ndi alembi; ndipo anapita naye kubwalo lao,
Pakuti zoonadi anasonkhanidwa m'mzinda muno Herode, ndi Pontio Pilato yemwe pamodzi ndi amitundu ndi anthu a Israele kumchitira choipa Mwana wanu wopatulika Yesu amene munamdzoza;