Ndipo Iye anayamba kulankhula nao m'mafanizo. Munthu analima munda wampesa, nauzunguniza ndi linga, nakumba moponderamo mphesa, namanga nsanja, naukongoletsa kwa olima munda, namuka kwina.
Luka 22:9 - Buku Lopatulika Ndipo iwo ananena naye, Mufuna tikakonzere kuti? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iwo ananena naye, Mufuna tikakonzere kuti? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma iwo adamufunsa kuti, “Kodi tikakonzere kuti?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo anafunsa kuti, “Kodi mukufuna tikakonzere kuti?” |
Ndipo Iye anayamba kulankhula nao m'mafanizo. Munthu analima munda wampesa, nauzunguniza ndi linga, nakumba moponderamo mphesa, namanga nsanja, naukongoletsa kwa olima munda, namuka kwina.
Ndipo Iye anati kwa iwo, Onani, mutalowa m'mzinda, adzakomana ndinu munthu alikusenza mtsuko wa madzi; mumtsate ameneyo kunyumba kumene akalowako iye.