Ndipo Yeremiya anati kwa Zedekiya, Ndikakufotokozerani, kodi simudzandipha ine? Ndipo ndikakupangirani, simudzandimvera ine.
Luka 22:68 - Buku Lopatulika ndipo ndikakufunsani kanthu, simudzayankha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo ndikakufunsani kanthu, simudzayankha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndipo nditakufunsani funso, inu simungaliyankhe. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ine nditakufunsani inu, simungandiyankhe. |
Ndipo Yeremiya anati kwa Zedekiya, Ndikakufotokozerani, kodi simudzandipha ine? Ndipo ndikakupangirani, simudzandimvera ine.
Koma kuyambira tsopano Mwana wa Munthu adzakhala padzanja lamanja la mphamvu ya Mulungu.