Ndipo iwo anagwidwa ndi chisoni chachikulu, nayamba kunena kwa Iye mmodzimmodzi, Kodi ndine, Ambuye?
Luka 22:23 - Buku Lopatulika Ndipo anayamba kufunsana mwa iwo okha, ndiye yani mwa iwo amene adzachita ichi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anayamba kufunsana mwa iwo okha, ndiye yani mwa iwo amene adzachita ichi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Apo onse adayamba kumafunsana kuti, “Kodi ndani mwa ife angachite zotere?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo anayamba kufunsana pakati pawo kuti ndi ndani wa iwo amene akanachita ichi. |
Ndipo iwo anagwidwa ndi chisoni chachikulu, nayamba kunena kwa Iye mmodzimmodzi, Kodi ndine, Ambuye?
Pakuti Mwana wa Munthu amukatu, monga kunaikidwiratu; koma tsoka munthuyo amene ampereka!