mabwenzi anga enieni onse anyansidwa nane; ndi onse ndakondana nao asandulika adani anga.
Luka 22:21 - Buku Lopatulika Koma onani, dzanja lake la iye amene adzandipereka ali pagome pano pamodzi ndi Ine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma onani, dzanja lake la iye amene adzandipereka ali pagome pano pamodzi ndi Ine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Koma ndithudi wondipereka kwa adani akudya nane pamodzi pompano. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma dzanja la amene akundipereka Ine lili pamodzi ndi langa pa chakudya pano. |
mabwenzi anga enieni onse anyansidwa nane; ndi onse ndakondana nao asandulika adani anga.
Ngakhale bwenzi langa lenileni, amene ndamkhulupirira, ndiye amene adadyako mkate wanga, anandikwezera chidendene chake.
Ndipo Yesu anayankha, Ndi iyeyu, amene Ine ndidzamsunsira nthongo ndi kumpatsa. Pamenepo, m'mene anasunsa nthongo anaitenga naipatsa Yudasi mwana wa Simoni Iskariote.