Ndipo pakufika madzulo, Iye analinkukhala pachakudya pamodzi ndi ophunzira khumi ndi awiri;
Luka 22:14 - Buku Lopatulika Ndipo itadza nthawi yake, Iye anakhala pachakudya, ndi ophunzira pamodzi ndi Iye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo itadza nthawi yake, Iye anakhala pachakudya, ndi ophunzira pamodzi ndi Iye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Nthaŵi itakwana, Yesu adakakhala podyera pamodzi ndi atumwi ake aja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ora litakwana, Yesu ndi ophunzira ake anakhala pa tebulo. |
Ndipo pakufika madzulo, Iye analinkukhala pachakudya pamodzi ndi ophunzira khumi ndi awiri;
Ndipo atumwi anasonkhana kwa Yesu; namuuza zilizonse adazichita, ndi zonse adaziphunzitsa.
Ndipo anati kwa iwo, Ndinalakalaka ndithu kudya Paska uwu pamodzi ndinu, ndisanayambe kusautsidwa;