Ndidzanyamuka ndipite kwa atate wanga, ndipo ndidzanena naye, Atate, ndinachimwira Kumwamba ndi pamaso panu;
Luka 20:4 - Buku Lopatulika Ubatizo wa Yohane unachokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ubatizo wa Yohane unachokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa kodi Yohane Mbatizi kuti azibatiza, mphamvu zake adaazitenga kwa yani, kwa Mulungu kapena kwa anthu?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ‘Kodi ubatizo wa Yohane, unali wochokera kumwamba, kapena wochokera kwa anthu?’ ” |
Ndidzanyamuka ndipite kwa atate wanga, ndipo ndidzanena naye, Atate, ndinachimwira Kumwamba ndi pamaso panu;
Ndipo anatsutsana mwa okha, nanena, Ngati tinena uchokera Kumwamba; adzati, Simunamkhulupirire chifukwa ninji?