Pomwepo anati kwa wina, Ndipo iwe uli nao mangawa otani? Ndipo uyu anati, Madengu a tirigu zana. Iye ananena naye, Tenga kalata yako nulembere makumi asanu ndi atatu.
Luka 20:12 - Buku Lopatulika Ndipo anatumizanso wina wachitatu; ndipo iyenso anamlasa, namtaya kunja. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anatumizanso wina wachitatu; ndipo iyenso anamlasa, namtaya kunja. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adatumanso wachitatu, koma uyunso alimiwo adamuvulaza, namtaya kunja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye anatumizanso wina wachitatu ndipo iwo anamuvulaza namuponya kunja. |
Pomwepo anati kwa wina, Ndipo iwe uli nao mangawa otani? Ndipo uyu anati, Madengu a tirigu zana. Iye ananena naye, Tenga kalata yako nulembere makumi asanu ndi atatu.
Ndipo anatumizanso kapolo wina; ndipo iyenso anampanda, namchitira chipongwe, nambweza, wopanda kanthu.
Ndipo mwini mundawo anati, Ndidzachita chiyani? Ndidzatuma mwana wanga amene ndikondana naye; kapena akamchitira iye ulemu.