Luka 2:50 - Buku Lopatulika Ndipo sanadziwitse mau amene Iye analankhula nao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo sanadziwitse mau amene Iye analankhula nao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma iwo sadamvetse zimene adaŵayankhazo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma iwo sanazindikire chomwe Iye amatanthauza. |
Ndipo sanadziwitse kanthu ka izi; ndi mau awa adawabisikira, ndipo sanazindikire zonenedwazo.
Koma iwo sanadziwitse mau awa, ndipo anabisidwa kwa iwo, kuti asawadziwe; ndipo anaopa kumfunsa za mau awa.