koma iwo anayesa kuti Iye ali m'chipiringu cha ulendo, nayenda ulendo wa tsiku limodzi; ndipo anayamba kumfunafuna Iye mwa abale ao ndi mwa anansi ao;
Luka 2:45 - Buku Lopatulika ndipo pamene sanampeze, anabwera ku Yerusalemu, namfunafuna Iye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo pamene sanampeze, anabwera ku Yerusalemu, namfunafuna Iye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ataona kuti sakumpeza, adabwerera ku Yerusalemu akumufunafuna ndithu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atalephera kumupeza, anabwerera ku Yerusalemu kukamufuna. |
koma iwo anayesa kuti Iye ali m'chipiringu cha ulendo, nayenda ulendo wa tsiku limodzi; ndipo anayamba kumfunafuna Iye mwa abale ao ndi mwa anansi ao;
Ndipo pakupita masiku atatu, anampeza Iye mu Kachisi, analikukhala pakati pa aphunzitsi, namva iwo, nawafunsanso mafunso.