Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa ine, tili zizindikiro ndi zodabwitsa mwa Israele, kuchokera kwa Yehova wa makamu, amene akhala m'phiri la Ziyoni.
Luka 2:18 - Buku Lopatulika Ndipo anthu onse amene anamva anazizwa ndi zinthu abusa adalankhula nao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anthu onse amene anamva anazizwa ndi zinthu abusa adalankhula nao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Onse amene ankamva, ankadabwa ndi zimene abusawo ankaŵasimbira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo onse amene anamva zimene abusawa ananena anadabwa. |
Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa ine, tili zizindikiro ndi zodabwitsa mwa Israele, kuchokera kwa Yehova wa makamu, amene akhala m'phiri la Ziyoni.
Ndipo anthu onse anadabwa, nalankhulana wina ndi mnzake, nanena, Mau amenewa ali otani? Chifukwa ndi ulamuliro ndi mphamvu angolamulira mizimu yonyansa, ndipo ingotuluka.