kotero kuti mukakhale ana a Atate wanu wa Kumwamba; chifukwa Iye amakwezera dzuwa lake pa oipa ndi pa abwino, namavumbitsira mvula pa olungama ndi pa osalungama.
Luka 18:6 - Buku Lopatulika Ndipo Ambuye anati, Tamverani chonena woweruza wosalungama. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Ambuye anati, Tamverani chonena woweruza wosalungama. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Ambuye adati, “Mwamvatu mau a woweruza wosalungama uja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Ambuye anati, “Tamvani zimene woweruza wopanda chilungamoyu wanena. |
kotero kuti mukakhale ana a Atate wanu wa Kumwamba; chifukwa Iye amakwezera dzuwa lake pa oipa ndi pa abwino, namavumbitsira mvula pa olungama ndi pa osalungama.
Ndipo pamene Ambuye anamuona, anagwidwa ndi chifundo chifukwa cha iye, nanena naye, Usalire.
Ndipo Yohane anaitana awiri a ophunzira ake, nawatuma kwa Ambuye, nanena, Kodi ndinu wakudzayo, kapena tiyang'anire wina?