Ndipo Yesu anaima, nalamulira kuti abwere naye kwa Iye; ndipo m'mene adafika pafupi, anamfunsa iye,
Luka 18:41 - Buku Lopatulika Ufuna ndikuchitire chiyani? Ndipo anati, Ambuye, kuti ndipenyenso. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ufuna ndikuchitire chiyani? Ndipo anati, Ambuye, kuti ndipenyenso. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Kodi ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?” Iye adati, “Ambuye, ndikufuna kuti ndizipenyanso.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Kodi ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?” Iye anayankha kuti, “Ambuye, ine ndifuna ndionenso.” |
Ndipo Yesu anaima, nalamulira kuti abwere naye kwa Iye; ndipo m'mene adafika pafupi, anamfunsa iye,
Musadere nkhawa konse; komatu m'zonse ndi pemphero, ndi pembedzero, pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.