ndipo sadzanena, Taonani uwu, kapena uwo! Pakuti, taonani, Ufumu wa Mulungu uli m'kati mwa inu.
Luka 17:23 - Buku Lopatulika Ndipo adzanena ndi inu, Taonani ilo! Taonani ili? Musachoka kapena kuwatsata; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo adzanena ndi inu, Taonani ilo! Taonani ili? Musachoka kapena kuwatsata; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu azidzakuuzani kuti, ‘Suuwo uli uko,’ kapena, ‘Suuwu uli pano,’ musadzapiteko kapena kuŵatsatira ai. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu adzakuwuzani kuti, ‘Uyo ali apoyo!’ kapena ‘Uyu ali apa!’ Musawathamangire iwo. |
ndipo sadzanena, Taonani uwu, kapena uwo! Pakuti, taonani, Ufumu wa Mulungu uli m'kati mwa inu.
Ndipo Iye anati, Yang'anirani musasocheretsedwe; pakuti ambiri adzadza m'dzina langa, nadzanena, Ndine amene; ndipo, Nthawi yayandikira; musawatsate pambuyo pao.