Pakuti monga ana a Yonadabu mwana wa Rekabu achita lamulo la kholo lao limene anawauza, koma anthu awa sanandimvere Ine.
Luka 15:11 - Buku Lopatulika Ndipo Iye anati, Munthu wina anali ndi ana aamuna awiri; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Iye anati, Munthu wina anali ndi ana amuna awiri; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu adatinso, “Munthu wina adaali ndi ana aamuna aŵiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yesu anapitiriza kunena kuti, “Panali munthu amene anali ndi ana aamuna awiri. |
Pakuti monga ana a Yonadabu mwana wa Rekabu achita lamulo la kholo lao limene anawauza, koma anthu awa sanandimvere Ine.
Chomwecho, ndinena kwa inu, kuli chimwemwe pamaso pa angelo a Mulungu chifukwa cha munthu wochimwa mmodzi amene atembenuka mtima.
ndipo wamng'onoyo anati kwa atate wake, Atate, ndigawirenitu zanga za pa chuma chanu. Ndipo iye anawagawira za moyo wake.