Luka 14:6 - Buku Lopatulika Ndipo iwo sanathe kumbwezera mau pa zinthu izi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iwo sanathe kumbwezera mau pa zinthu izi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Iwo adasoŵa poyankha. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo iwo analibe choyankha. |
Ndipo pamene Iye anatero, onse aja akutsutsana naye ananyazitsidwa; ndipo anthu onse a m'khamu anakondwera ndi zinthu zonse za ulemererozo zinachitidwa ndi Iye.
Ndipo sanakhoze kugwira mauwo pamaso pa anthu; ndipo anazizwa ndi kuyankha kwake, nakhala chete.
Pakuti Ine ndidzakupatsani inu kamwa ndi nzeru, zimene adani anu onse sadzatha kuzikana kapena kuzitsutsa.