Ndipo Yesu anayendayenda mu Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira Uthenga Wabwino wa Ufumu, nachiritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.
Luka 13:10 - Buku Lopatulika Ndipo analikuphunzitsa m'sunagoge mwina, tsiku la Sabata. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo analikuphunzitsa m'sunagoge mwina, tsiku la Sabata. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsiku lina la Sabata Yesu ankaphunzitsa m'nyumba ina yamapemphero. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa Sabata Yesu ankaphunzitsa mʼsunagoge ina, |
Ndipo Yesu anayendayenda mu Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira Uthenga Wabwino wa Ufumu, nachiritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.
ndipo ngati udzabala chipatso kuyambira pamenepo, chabwino; koma ngati iai, mudzaulikhatu.