Pamenepo ndinadula ndodo yanga ina, ndiyo Chomanganitsa, kuti ndithetse chibale cha pakati pa Yuda ndi Israele.
Luka 12:51 - Buku Lopatulika Kodi muyesa kuti ndinadzera kudzapatsa mtendere padziko lapansi? Ndinena kwa inu, Iaitu, komatu kutsutsana; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Kodi muyesa kuti ndinadzera kudzapatsa mtendere pa dziko lapansi? Ndinena kwa inu, Iaitu, komatu kutsutsana; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kodi mukuyesa kuti ndidadzapereka mtendere pansi pano? Iyai, kunena zoona, osati mtendere koma kugaŵikana. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kodi mukuganiza kuti Ine ndinabwera kudzabweretsa mtendere pa dziko lapansi? Ayi, Ine ndikukuwuzani kuti, ndinabweretsa kugawikana. |
Pamenepo ndinadula ndodo yanga ina, ndiyo Chomanganitsa, kuti ndithetse chibale cha pakati pa Yuda ndi Israele.
pakuti kuyambira tsopano adzakhala m'nyumba imodzi anthu asanu, atatu adzatsutsana ndi awiri, ndi awiri adzatsutsana ndi atatu.