Luka 12:34 - Buku Lopatulika Pakuti kumene kuli chuma chanu, komweko kudzakhalanso mtima wanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti kumene kuli chuma chanu, komweko kudzakhalanso mtima wanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pajatu kumene kuli chuma chako, mtima wakonso kokhala nkomweko.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Popeza kumene kuli chuma chanu, mtima wanunso udzakhala komweko.” |
Pakuti ufulu wathu uli Kumwamba; kuchokera komwenso tilindirira Mpulumutsi, Ambuye Yesu Khristu;