Ndipo pakusonkhana pamodzi makamu a anthu, anayamba kunena, Mbadwo uno ndi mbadwo woipa; ufuna chizindikiro, ndipo chizindikiro sichidzapatsidwa kwa uwu koma chizindikiro cha Yona.
Luka 11:16 - Buku Lopatulika Koma ena anamuyesa, nafuna kwa Iye chizindikiro chochokera Kumwamba. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma ena anamuyesa, nafuna kwa Iye chizindikiro chochokera Kumwamba. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Enanso pofuna kumuyesa, adampempha kuti aŵaonetse chizindikiro chozizwitsa chochokera kumwamba. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ena anamuyesa pomufunsa chizindikiro chochokera kumwamba. |
Ndipo pakusonkhana pamodzi makamu a anthu, anayamba kunena, Mbadwo uno ndi mbadwo woipa; ufuna chizindikiro, ndipo chizindikiro sichidzapatsidwa kwa uwu koma chizindikiro cha Yona.
Chifukwa chake anati kwa Iye, Ndipo muchita chizindikiro chanji, kuti tione ndi kukhulupirira Inu? Muchita chiyani?
Koma ichi ananena kuti amuyese Iye, kuti akhale nacho chomneneza Iye. Koma Yesu, m'mene adawerama pansi analemba pansi ndi chala chake.