Koma m'mene iye anatulukamo, sanathe kulankhula nao; ndipo anazindikira kuti iye adaona masomphenya mu Kachisimo. Ndipo iye analinkukodola iwo, nakhalabe wosalankhula.
Luka 1:62 - Buku Lopatulika Ndipo anakodola atate wake, afuna amutche dzina liti? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anakodola atate wake, afuna amutche dzina liti? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono adalankhula ndi bambo wake ndi manja, namufunsa kuti, “Mukufuna kuti timutche dzina lanji?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamenepo anapanga zizindikiro kwa abambo ake kuti adziwe dzina limene akanakonda kumutcha mwanayo. |
Koma m'mene iye anatulukamo, sanathe kulankhula nao; ndipo anazindikira kuti iye adaona masomphenya mu Kachisimo. Ndipo iye analinkukodola iwo, nakhalabe wosalankhula.