Ndipo iwo anati kwa iye, Palibe wina wa abale ako amene atchedwa dzina ili.
Pamenepo anthuwo adamuuza kuti, “Koma pakati pa abale anu palibe amene ali ndi dzina limeneli.”
Iwo anati kwa iye, “Palibe mmodzi mwa abale ake amene ali ndi dzina limeneli.”
Ndipo amake anayankha, kuti, Iai; koma adzatchedwa Yohane.
Ndipo anakodola atate wake, afuna amutche dzina liti?
Kunali munthu, wotumidwa ndi Mulungu, dzina lake ndiye Yohane.