Luka 1:40 - Buku Lopatulika nalowa m'nyumba ya Zekariya, nalonjera Elizabeti. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 nalowa m'nyumba ya Zekariya, nalonjera Elizabeti. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adakaloŵa m'nyumba ya Zakariya, malonjera Elizabeti. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kumene anakalowa mʼnyumba ya Zakariya nalonjera Elizabeti. |
Ndipo Maria ananyamuka masiku amenewa, namuka ndi changu kudziko la mapiri kumzinda wa Yuda;
Ndipo panali pamene Elizabeti anamva kulonjera kwake kwa Maria, mwana wosabadwayo anatsalima m'mimba mwake; ndipo Elizabeti anadzazidwa ndi Mzimu Woyera;
Masiku a Herode, mfumu ya Yudeya, kunali munthu wansembe, dzina lake Zakariya, wa gulu la ansembe la Abiya; ndi mkazi wake wa ana aakazi a fuko la Aroni, dzina lake Elizabeti.