Ndi abale ao m'midzi mwao akafikafika, atapita masiku asanu ndi awiri masabata onse, kuti akhale nao;
Luka 1:23 - Buku Lopatulika Ndipo kunali, pamene masiku a utumiki wake anamalizidwa, anamuka kunyumba kwake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo kunali, pamene masiku a utumiki wake anamalizidwa, anamuka kunyumba kwake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Atatha masiku ake otumikira m'Nyumba ya Mulungu, adapita kwao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nthawi yake yotumikira itatha, anabwerera kwawo. |
Ndi abale ao m'midzi mwao akafikafika, atapita masiku asanu ndi awiri masabata onse, kuti akhale nao;
Koma m'mene iye anatulukamo, sanathe kulankhula nao; ndipo anazindikira kuti iye adaona masomphenya mu Kachisimo. Ndipo iye analinkukodola iwo, nakhalabe wosalankhula.