Nutenge mafuta onse akukuta matumbo, ndi chokuta cha mphafa ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pa izo, ndi kuzitentha paguwa la nsembe.
Levitiko 4:9 - Buku Lopatulika ndi impso ziwiri ndi mafuta ali pomwepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi impso ziwiri ndi mafuta ali pomwepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Achotsenso imso ziŵiri pamodzi ndi mafuta ake omwe cham'chiwunomu, ndiponso mphumphu za mafuta akuchiŵindi ochotsa pamodzi ndi imso zija, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Achotsenso ndi kubwera ndi impsyo zonse ziwiri pamodzi ndi mafuta onse ndiponso mafuta onse amene aphimba chiwindi ndi impsyo |
Nutenge mafuta onse akukuta matumbo, ndi chokuta cha mphafa ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pa izo, ndi kuzitentha paguwa la nsembe.
ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pomwepo okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso.
umo azikachotsera pa ng'ombe ya nsembe yoyamika; ndipo wansembe azitenthe paguwa la nsembe yopsereza.