Levitiko 3:5 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Aroni azitenthe paguwa la nsembe, pa nsembe yopsereza, ili pa nkhuni zimene zili pamoto; ndiyo nsembe yamoto, ya fungo lokoma la kwa Yehova.
Onani mutuwo
Ndipo ana a Aroni azitenthe pa guwa la nsembe, pa nsembe yopsereza, ili pa nkhuni zimene zili pamoto; ndiyo nsembe yamoto, ya fungo lokoma la kwa Yehova.
Onani mutuwo
Tsono ana a Aroni atenthe zonsezo pa guwa, pamodzi ndi nsembe yopsereza imene ili pa nkhuni pamotopo. Imeneyo ndiyo nsembe yotentha pa moto, ya fungo lokomera Chauta.
Onani mutuwo
Ndipo ana a Aaroni atenthe zimenezi pa guwa, pamwamba pa chopereka chopsereza chimene chili pa nkhuni zoyakazo. Imeneyi ndi nsembe yotentha pa moto, ya fungo lokomera Yehova.
Onani mutuwo