Levitiko 2:6 - Buku Lopatulika Uphwanye, nuthirepo mafuta; ndiyo nsembe yaufa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Uphwanye, nuthirepo mafuta; ndiyo nsembe yaufa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Umuduledule ndi kumupaka mafuta. Chimenecho ndicho chopereka cha chakudya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Umuduledule bulediyo ndi kumupaka mafuta; imeneyo ndi nsembe yachakudya. |
Ndipo nsembe yaufa yako ikakhala yokazinga m'chiwaya, ikhale ya ufa wosalala wopanda chotupitsa, wosakaniza ndi mafuta.
Ndipo chopereka chako chikakhala nsembe yaufa ya mumphika, chikhale cha ufa wosalala ndi mafuta.