Genesis 9:28 - Buku Lopatulika Ndipo Nowa anakhala ndi moyo chigumula chitapita, zaka mazana atatu kudza makumi asanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Nowa anakhala ndi moyo chigumula chitapita, zaka mazana atatu kudza makumi asanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chitatha chigumulacho, Nowa adakhala ndi moyo zaka zina 350. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Chitatha chigumula, Nowa anakhala ndi moyo zaka 350. |
Ndipo masiku onse a Nowa anali mazana asanu ndi anai kudza makumi asanu: ndipo anamwalira.