Mwezi wachiwiri tsiku la makumi awiri kudza asanu ndi awiri la mwezi, lidauma dziko lapansi.
Genesis 8:15 - Buku Lopatulika Mulungu ndipo ananena kwa Nowa, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mulungu ndipo ananena kwa Nowa, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mulungu adauza Nowa kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsono Mulungu anawuza Nowa kuti, |
Mwezi wachiwiri tsiku la makumi awiri kudza asanu ndi awiri la mwezi, lidauma dziko lapansi.
Tulukamoni m'chingalawamo, iwe ndi ana ako, ndi mkazi wako, ndi akazi a ana ako pamodzi ndi iwe.