Ndipo Mulungu anakumbukira Nowa ndi zamoyo zonse, ndi nyama zonse zimene zinali pamodzi naye m'chingalawamo; ndipo Mulungu anapititsa mphepo padziko lapansi, naphwa madzi;
Genesis 7:24 - Buku Lopatulika Ndipo anapambana madzi padziko lapansi masiku zana kudza makumi asanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anapambana madzi pa dziko lapansi masiku zana kudza makumi asanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Madziwo adakhala osaphwa konse pa dziko lapansi masiku 150. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Madziwo anadzaza dziko lonse lapansi kwa masiku 150. |
Ndipo Mulungu anakumbukira Nowa ndi zamoyo zonse, ndi nyama zonse zimene zinali pamodzi naye m'chingalawamo; ndipo Mulungu anapititsa mphepo padziko lapansi, naphwa madzi;