Genesis 6:10 - Buku Lopatulika Ndipo Nowa anabala ana aamuna atatu: Semu, Hamu ndi Yafeti. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Nowa anabala ana amuna atatu, Semu, Hamu ndi Yafeti. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anali ndi ana aamuna atatu: Semu, Hamu ndi Yafeti. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nowa anabereka ana aamuna atatu: Semu, Hamu ndi Yafeti. |
Ndipo dziko lapansi linavunda pamaso pa Mulungu, dziko lapansi ndipo linadzala ndi chiwawa.
Mibadwo ya Nowa ndi iyi: Nowa anali munthu wolungama ndi wangwiro m'mibadwo yake; Nowa anayendabe ndi Mulungu.