Ndipo pamene abale ake a Yosefe anaona kuti atate wao anafa, anati, Kapena Yosefe adzatida ife, ndipo adzatibwezera ife zoipa zonse tidamchitira iye.
Genesis 50:16 - Buku Lopatulika Ndipo anatumiza mthenga kwa Yosefe kuti, Atate wathu asanafe analamulira, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anatumiza mthenga kwa Yosefe kuti, Atate wathu asanafe analamulira, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero adatumiza mau kwa Yosefe kuti, “Atate anu asanafe adanena mau akuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Motero anatumiza mawu kwa Yosefe kuti, “Abambo anu anasiya malangizo asanafe nati: |
Ndipo pamene abale ake a Yosefe anaona kuti atate wao anafa, anati, Kapena Yosefe adzatida ife, ndipo adzatibwezera ife zoipa zonse tidamchitira iye.
Muziti chotero kwa Yosefe, Mukhululukiretu tsopano kulakwa kwa abale anu, ndi kuchimwa kwao, chifukwa kuti anakuchitirani inu choipa; tsopano mutikhululukiretu kulakwa kwa akapolo a Mulungu wa atate wanu. Ndipo Yosefe analira pamene iwo ananena ndi iye.