ndipo Lameki anakhala ndi moyo atabala Nowa, zaka mazana asanu kudza makumi asanu ndi anai ndi zisanu, nabala ana aamuna ndi aakazi:
Genesis 5:31 - Buku Lopatulika masiku ake onse a Lameki anali zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamwalira. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 masiku ake onse a Lameki anali zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamwalira. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adamwalira ali wa zaka 777. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zaka zonse za Lameki zinali 777, ndipo kenaka anamwalira. |
ndipo Lameki anakhala ndi moyo atabala Nowa, zaka mazana asanu kudza makumi asanu ndi anai ndi zisanu, nabala ana aamuna ndi aakazi: