Genesis 49:32 - Buku Lopatulika munda ndi phanga lili m'menemo, zinagulidwa kwa ana a Hiti Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 munda ndi phanga lili m'menemo, zinagulidwa kwa ana a Hiti Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mundawo pamodzi ndi phangalo adagula kwa Ahiti.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Munda ndi manda amene ali mʼmenemo zinagulidwa kwa Ahiti.” |
pamenepo anaika Abrahamu ndi Sara mkazi wake; pamenepo anaika Isaki ndi Rebeka mkazi wake: pamenepo ndinaika Leya:
Pamene Yakobo anatha kulangiza ana ake aamuna, anafunya mapazi ake pakama, natsirizika, nasonkhanitsidwa kwa anthu a mtundu wake.