Adamanga mwana wa kavalo wake pampesa, ndi mwana wa bulu wake pa mpesa wosankhika; natsuka malaya ake m'vinyo, ndi chofunda chake m'mwazi wa mphesa.
Genesis 49:12 - Buku Lopatulika Maso ake adzafiira ndi vinyo, ndipo mano ake adzayera ndi mkaka. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Maso ake adzafiira ndi vinyo, ndipo mano ake adzayera ndi mkaka. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Maso ake ndi ofiira ndi vinyo mano ake ndi oyera ndi mkaka. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Maso ake adzakhala akuda chifukwa cha vinyo, mano ake woyera chifukwa cha mkaka. |
Adamanga mwana wa kavalo wake pampesa, ndi mwana wa bulu wake pa mpesa wosankhika; natsuka malaya ake m'vinyo, ndi chofunda chake m'mwazi wa mphesa.
Zebuloni adzakhala m'mphepete mwa nyanja; ndipo iye adzakhala dooko la ngalawa; ndipo malire ake adakhala pa Sidoni.
Ndani ali ndi chisoni? Ndani asauka? Ndani ali ndi makangano? Ndani ang'ung'udza? Ndani alasidwa chabe? Ndani afiira maso?