Nuike chikho changa, chikho chasiliva chija, kukamwa kwa thumba la wamng'ono, pamodzi ndi ndalama za tirigu zake. Ndipo iye anachita monga mau ananena Yosefe.
Genesis 44:3 - Buku Lopatulika Pamene kudacha, anamukitsa anthu iwo ndi abulu ao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamene kudacha, anamukitsa anthu iwo ndi abulu ao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'maŵa kutacha, anthu aja adaloledwa kupita pamodzi ndi abulu ao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mmawa kutacha anthu aja analoledwa kuti apite ndi abulu awo. |
Nuike chikho changa, chikho chasiliva chija, kukamwa kwa thumba la wamng'ono, pamodzi ndi ndalama za tirigu zake. Ndipo iye anachita monga mau ananena Yosefe.
Atatuluka m'mzinda asanamuke patali, Yosefe anati kwa tsanyumba wake, Tanyamuka, talondola anthu aja, ukawapeza unene nao, Chifukwa chanji mwabwezera zoipa m'malo mwa zabwino?